Isaiah 48:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana ako akadachuluka ngati mchenga, ndipo zidzukulu zako ngati fumbi. Dzina lao silikadachotsedwa pamaso panga, silikadafafanizika konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mbeu yakonso ikadakhala monga mchenga, ndi obadwa a m'chuuno mwako momwemo; dzina lake silikadachotsedwa, pena kuonongeka pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzukulu zako zikanachuluka ngati mchenga, ana ako akanachuluka ngati fumbi; dzina lawo silikanachotsedwa pamaso panga ndipo silikanafafanizidwa konse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
mbeu yakonso ikadakhala monga mcenga ndi obadwa a m'cuuno mwako momwemo; dzina lace silikadacotsedwa, pena kuonongeka pamaso panga.