Isaiah 48:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe inu mukunyada kuti ndinu nzika za mzinda wopatulika ndipo kuti mumakhulupirira Mulungu wa Israele, amene dzina lake ndi Chauta Wamphamvuzonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti adziyesa okha a mudzi wopatulika, ndi kudzikhazikitsa iwo okha pa Mulungu wa Israele; dzina lake ndi Yehova wa makamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe inu mumadzitcha nzika za mzinda wopatulika ndipo mumadalira Mulungu wa Israeli, amene dzina lake ndi Yehova Wamphamvuzonse:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti adziyesa okha a mudzi wopatulika, ndi kudzikhazikitsa iwo okha pa Mulungu wa Israyeli; dzina lace ndi Yehova wa makamu.