Isaiah 48:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaadziŵa kuti ndiwe wokanika, wa nkhongo gwa, ndi wa mutu wouma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza ndinadziwa, kuti uli wokanika, ndi khosi lako lili mtsempha wachitsulo, ndi mphumi yako mkuwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Ine ndinadziwa kuti iwe ndiwe nkhutukumve wa nkhongo gwaa, wa mutu wowuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza ndinadziwa, kuti uli wokanika, ndi khosi lako liri mtsempha wacitsulo, ndi mphumi yako mkuwa;