Isaiah 49:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe Yerusalemu, ndidadinda chithunzi chako pa zikhatho zanga, zipupa zako ndimakhala ndikuziwona nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taona ndakulembera iwe pa zikhato za manja anga; makoma ako alipo masiku onse pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Taona, ndakulemba iwe mʼzikhantho zanga; makoma ako ndimawaona nthawi zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taona ndakulembera iwe pa zikhato za manja anga; makoma ako alipo masiku onse pamaso panga,