Isaiah 49:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adasandutsa pakamwa panga kuti pakhale ngati lupanga lakuthwa. Adanditchinjiriza ndi dzanja lake. Adandisula ngati muvi wakuthwa, nandibisa m'phodo mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nachititsa pakamwa panga ngati lupanga lakuthwa, mu mthunzi wa dzanja lake wandibisa Ine; wandipanga Ine; muvi wotuulidwa; m'phodo mwake Iye wandisungitsa Ine, nati kwa Ine,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anasandutsa pakamwa panga kukhala ngati lupanga lakuthwa, anandibisa mu mthunzi wa dzanja lake; Iye anandisandutsa ngati muvi wakuthwa ndipo anandibisa mʼchimake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nacititsa pakamwa panga ngati lupanga lakuthwa, mu mthunzi wa dzanja lace wandibisa Ine; wandipanga Ine mubvi wotuulidwa; m'phodo mwace Iye wandisungitsa Ine, nati kwa Ine,