Isaiah 49:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandiwuza kuti, “Iwe Israele ndiwe mtumiki wanga. Anthu adzanditamanda chifukwa cha iwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe ndiwe mtumiki wanga, Israele, amene ndidzalemekezedwa nawe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anati kwa ine, “Ndiwe mtumiki wanga, Israeli. Anthu adzanditamanda chifukwa cha iwe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe ndiwe mtumiki wanga, Israyeli, amene ndidzalemekezedwa nawe.