Isaiah 49:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzauza am'ndende kuti atuluke, ndi amene ali mu mdima kuti aonekere poyera. Adzapeza chakudya m'mphepete mwa njira, adzapeza busa pa magomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kunena kwa iwo amene ali omangidwa, Mukani, kwa iwo amene ali mumdima, Dzionetseni nokha. Iwo adzadya m'njira, ndi m'zitunda zonse zoti see mudzakhala busa lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawuza a mʼndende kuti atuluke ndi a mu mdima kuti aonekere poyera. “Adzapeza chakudya mʼmphepete mwa njira ndi msipu pa mʼmalo owuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kunena kwa iwo amene ali omangidwa, Mukani, kwa iwo amene ali mumdima, Dzionetseni nokha. Iwo adzadya m'njira, ndi m'zitunda zonse zoti se mudzakhala busa lao.