Isaiah 5:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntamuimbirako bwenzi langa nyimbo yokamba za wokondedwa wanga ndi munda wake wamphesa. Wokondedwa wanga anali ndi munda wamphesa pa phiri la nthaka yachonde.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiimbire wokondedwa wanga nyimbo ya wokondedwa wanga ya munda wake wamphesa. Wokondedwa wanga anali ndi munda wamphesa m'chitunda cha zipatso zambiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzamuyimbira bwenzi langa nyimbo yokamba za munda wake wa mpesa: Wokondedwa wanga anali ndi munda wamphesa pa phiri la nthaka yachonde.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiyimbire wokondedwa wanga nyimbo ya wokondedwa wanga ya munda wace wamphesa, Wokondedwa wanga anali ndi munda wamphesa m'citunda ca zipatso zambiri;