Isaiah 5:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munda wamphesa wa mahekitara khumi, vinyo wake adzangodzaza mbiya imodzi. Kufesa madengu khumi a mbeu, zokolola zake zidzangodzaza dengu limodzi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa kuti munda wamphesa wa madera khumi udzangobala bati imodzi ya vinyo, ndi mbeu za maefa khumi zidzangobala efa imodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munda wamphesa wa maekala khumi udzatulutsa vinyo wodzaza mbiya imodzi, kufesa madengu khumi a mbewu, zokolola zake zidzangodzaza dengu limodzi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa kuti munda wamphesa wa madera khumi udzangobala mbiya imodzi, ndi mbeu za nsengwa khumi zidzangobala nsengwa imodzi.