Isaiah 5:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anaankhosa adzadya pamenepo ngati pabusa pao, ndipo anaambuzi adzadya m'mabwinja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anaankhosa adzadyapo ngati m'busa mwao, ndi malo a bwinja a zonenepa zachilendo zidzadyapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono nkhosa zidzadya pamenepo ngati pabusa pawo; ana ankhosa adzadya mʼmabwinja a anthu olemera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ana a nkhosa adzadyapo ngati m'busa mwao, ndi malo a bwinja a zonenepa zacilendo zidzadyapo.