Isaiah 5:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amanena kuti, “Chauta afulumire, agwire ntchito yake mwamsanga, kuti ntchitoyo tiiwone. Zimene Woyera uja wa Israele afuna kuchita, zichitiketu kuti tizidziŵe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene ati, Mlekeni iye akangaze, mlekeni iye afulumize ntchito yake kuti ife tione; ndipo lekani uphungu wa Woyera wa Israele uyandikire, udze kuti tiudziwe!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene amanena kuti, “Yehova afulumire, agwire ntchito yake mwamsanga kuti ntchitoyo tiyione. Ntchito zionekere, zimene Woyerayo wa Israeli akufuna kuchita, zichitike kuti tizione.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene ati, Mlekeni iye akangaze, mlekeni iye afulumize nchito yace kuti ife tione; ndipo lekani uphungu wa Woyera wa Israyeli uyandikire, udze kuti tiudziwe!