Isaiah 5:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa zidakwa zimene zimaika mtima pa vinyo! Tsoka kwa anthu amene saopa konse kusakaniza zakumwa zaukali!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka kwa iwo amene ali a mphamvu yakumwa vinyo, ndi anthu olimba akusanganiza zakumwa zaukali;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka kwa zidakwa zimene zimayika mtima pa vinyo ndipo ndi akatswiri posakaniza zakumwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka kwa iwo amene ali a mphamvu yakumwa vinyo, ndi anthu olimba akusanganiza zakumwa zaukali;