Isaiah 5:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalungamitsa wolakwa chifukwa cha chiphuphu nkuipitsa mlandu wa munthu wosalakwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene alungamitsa woipa pa chokometsera mlandu, nachotsera wolungama chilungamo chake!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene amamasula olakwa chifukwa cha chiphuphu koma amayipitsa mlandu wa munthu wosalakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene alungamitsa woipa pa cokometsera mlandu, nacotsera wolungama cilungamo cace!