Isaiah 5:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe ndi mmodzi yemwe wodzatopa kapena kukhumudwa, kuwodzera kapena kugona. Palibe lamba wam'chiwuno amene adzamasuke, palibe chingwe cha nsapato zao chimene chidzaduke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
palibe amene adzalema, kapena adzaphunthwa mwa iwo, palibe amene adzaodzera kapena kugona tulo; ngakhale lamba la m'chuuno mwao silidzamasuka, kapena chomangira cha nsapato zao sichidzaduka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe ndi mmodzi yemwe amene akutopa kapena kupunthwa, palibe amene akusinza kapena kugona; palibe lamba wa mʼchiwuno amene akumasuka, palibe chingwe cha nsapato chimene chaduka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
palibe amene adzalema, kapena adzapunthwa mwa iwo, palibe amene adzaodzera kapena kugona tulo; ngakhale lamba la m'cuuno mwao silidzamasuka, kapena comangira ca nsapato zao sicidzaduka;