Isaiah 5:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsoka kwa amene amangokhalira kulumikiza nyumba amene amangokhalira kuwonjezera minda, mpaka kulanda malo onse, kuti dziko lonse likhale la iwo okha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka kwa iwo amene aphatikiza nyumba ndi nyumba, amene alumikiza munda ndi munda, kufikira padzapanda malo, ndipo inu mudzasiyidwa nokha pakati pa dziko!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsoka kwa inu amene mumangokhalira kulumikiza nyumba, ndipo mumangokhalira kuwonjezera minda, mpaka mutalanda malo onse kuti muzikhalamo nokha mʼdzikomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka kwa iwo amene aphatikiza nyumba ndi nyumba, amene alumikiza munda ndi munda, kufikira padzapanda malo, ndipo inu mudzasiyidwa nokha pakati pa dziko!