Isaiah 50:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye Chauta ndi amene amandithandiza, ndani anganene kuti ndine wopalamula? Ndithu, onse ondizenga mlandu adzatheratu. Kutha kwake ngati chovala chodyewa ndi njenjete.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, Ambuye Yehova adzathandiza Ine; ndani amene adzanditsutsa? Taonani, iwo onse adzatha ngati chovala, njenjete zidzawadya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye Yehova ndiye amene amandithandiza. Ndaninso amene adzanditsutsa? Onse adzatha ngati chovala chodyedwa ndi njenjete.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, Ambuye Yehova adzathandiza Ine; ndani amene adzanditsutsa? taonani, iwo onse adzatha ngati cobvala, njenjete zidzawadya.