Isaiah 51:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndine Chauta, Mulungu wanu, amene ndimavundula nyanja, kotero kuti mafunde ake amakokoma. Dzina langa ndine Chauta Wamphamvuzonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Ine ndine Yehova Mulungu wako, amene ndiutsa nyanja, kuti mafunde ake akokome; Yehova wa makamu ndi dzina lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndimavundula nyanja kotero mafunde ake amakokoma. Dzina lake ndi Yehova Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Ine ndine Yehova Mulungu wako, amene ndiutsa nyanja, kuti mafunde ace akokome; Yehova wa makamu ndi dzina lace.