Isaiah 52:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Sadalandirepo kanthu pokugulitsani, choncho mudzaomboledwa osaperekapo ndalama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atero Yehova, Inu munagulitsidwa chabe, ndipo mudzaomboledwa opanda ndalama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova akuti, “Sindinalandirepo kanthu pamene ndinakugulitsani, choncho mudzawomboledwa wopanda ndalama.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atero Yehova, Inu munagulitsidwa cabe, ndipo mudzaomboledwa opanda ndalama.