Isaiah 52:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kale inu anthu anga mudaapita ku Ejipito kukakhala nao kumeneko, ndipo Aasiriya adaakuzunzani popanda chifukwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Ambuye Yehova atero, Anthu anga ananka ku Ejipito poyamba paja, kukakhala kumeneko; ndipo Asiriya anawatsendereza popanda chifukwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Ambuye Yehova akuti, “Poyamba paja anthu anga anapita kukakhala ku Igupto; nawonso Asiriya awapondereza popanda chifukwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Ambuye Yehova atero, Anthu anga ananka ku Aigupto poyamba paja, kukakhala kumeneko; ndipo Asuri anawatsendereza popanda cifukwa.