Isaiah 52:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo inu anthu anga mudzandidziŵa, nthaŵi imeneyo mudzadziŵa kuti ndine amene ndikulankhula. Ndithu ndinedi!’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake anthu anga adzadziwa dzina langa; chifukwa chake tsiku limenelo iwo adzadziwa kuti Ine ndine amene ndinena; taonani, ndine pano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono tsiku limenelo anthu anga adzadziwa dzina langa; kotero adzadziwa kuti ndi Ine amene ndikuyankhula, Indedi, ndine.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace anthu anga adzadziwa dzina langa; cifukwa cacersiku limenelo iwo adzadziwa kuti Ine ndine amene ndinena; taonani, ndine pano.