Isaiah 53:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndani wazikhulupirira zimene tamvazi? Ndani wazindikira mphamvu za Chauta pa zimenezi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani wamvera uthenga wathu? Ndi mkono wa Yehova wavumbulukira yani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani wakhulupirira zimene tanenazi; kapena ndani amene Yehova wamuzindikiritsa mphamvu zake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani wamvera uthenga wathu? Ndi mkono wa Yehova wabvumbulukira yani?