Isaiah 54:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akunena kuti, “Iwe Yerusalemu ndiwe mzinda wozunzika, wosoŵa chithandizo, wopanda wokutonthoza. Ndidzakongoletsa miyala yako, ndidzamanganso maziko ako ndi miyala ya mtengo wapatali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe wosautsidwa, wobelukabeluka ndi namondwe, wosatonthola mtima, taona, ndidzakhazika miyala yako m'mawangamawanga abwino, ndi kukhazika maziko ako ndi masafiro.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iwe mzinda wozunzika, wokunthidwa ndi namondwe ndiponso wopanda wokutonthoza, Ine ndidzakongoletsa miyala yako. Maziko ako ndidzamanga ndi miyala ya safiro.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe wosautsidwa, wobelukabeluka ndi namondwe, wosatonthola mtima, taona, ndidzakhazika miyala yako m'maanga-maanga abwino, ndi kukhazika maziko ako ndi masafiro.