Isaiah 54:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe Israele, Chauta wakuitananso. Uli ngati msungwana wosiyidwa, amene ali wodzaza ndi chisoni mu mtima, ngati mkazi wapaunyamata amene wachotsedwa, akuterotu Mulungu wako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova wakuitana iwe monga mkazi wakusiyidwa ndi wosauka m'mzimu, ngakhale mkazi wa ubwana wochotsedwa, ati Mulungu wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova wakuyitananso, uli ngati mkazi wosiyidwa ndi wodzaza ndi chisoni mu mtima, mkazi amene anakwatiwa pa unyamata wake kenaka nʼkukanidwa,” akutero Mulungu wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova wakuitana iwe monga mkazi wakusiyidwa ndi wosauka m'mzimu, ngakhale mkazi wa ubwana wocotsedwa, ati Mulungu wako.