Isaiah 54:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndidaakusiya pa kamphindi kochepa, koma ndidzakutenganso ndi chikondi chachikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kamphindi kakang'ono ndakusiya iwe, koma ndi chifundo chambiri ndidzakusonkhanitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kwa kanthawi kochepa, Ine ndinakusiya, koma ndidzakutenganso chifukwa ndimakukonda kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kamphindi kakang'ono ndakusiya iwe, koma ndi cifundo cambiri ndidzakusonkhanitsa.