Isaiah 56:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, amene amasonkhanitsa Aisraele onse obalalika, akunena kuti, “Ndidzasonkhanitsanso anthu ena kuwonjezera pa amene adasonkhana kale.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambuye Yehova amene asonkhanitsa otayika a Israele ati, Komabe ndidzasonkhanitsa ena kwa iye, pamodzi ndi osonkhanitsidwa akeake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye Yehova, amene amasonkhanitsa Aisraeli onse ali ku ukapolo akunena kuti, “Ndidzasonkhanitsano anthu ena kuwonjezera amene anasonkhana kale.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambuye Yehova amene asonkhanitsa otayika a Israyeli ati, Komabe ndidzasonkhanitsa ena kwa iye, pamodzi ndi osonkhanitsidwa ace ace.