Isaiah 57:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Kodi ndi milungu yanji imene mudaiwona nkuchita nayo mantha, kotero kuti mudandinamiza nkundiiŵaliratu, osalabada konse za Ine? Kodi mwaleka kundiwopa chifukwa choti ndakhala chete pa nthaŵi yaitali?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndi yani amene wamuopa ndi kuchita naye mantha, kuti wanama, osandikumbukira Ine, kapena kundisamalira? Kodi Ine sindinakhala chete nthawi yambiri, ndipo iwe sunandiopa Ine konse?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi ndani amene mwachita naye mantha ndi kumuopa, kotero kuti mwakhala mukundinamiza, ndipo Ine simundikumbukira nʼkomwe, kapena kuganizirapo mʼmitima yanu za Ine? Kodi mwaleka kundiopa chifukwa choti ndakhala chete nthawi yayitali?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndi yani amene wamuopa ndi kucita naye mantha, kuti wanama, osandikumbukira Ine, kapena kundisamalira? Kodi Ine sindinakhala cete nthawi yambiri, ndipo iwe sunandiopa Ine konse?