Isaiah 57:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukuganiza kuti zimene mumachita nzolungama, koma makhalidwe anu ndidzaŵaonetsa poyera, ndipo mafano sadzakuthandizani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzaonetsa chilungamo chako ndi ntchito zako sudzapindula nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ndaonetsa poyera ntchito zanu zomwe mumati nʼzolungama, ndi mafano anu kuti nʼzosathandiza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzaonetsa cilungamo cako ndi nchito zako sudzapindula nazo.