Isaiah 57:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Padzamveka mau akuti, “Lambulani, lambulani ndi kukonza mseu. Chotsani chitsa chilichonse pa njira yodzeramo anthu anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzanena, Undani, undani, konzani njira, chotsani chokhumudwitsa m'njira mwa anthu anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo panamveka mawu akuti, “Undani, undani, konzani msewu! Chotsani zotchinga pa njira yoyendamo anthu anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzanena, Undani, undani, konzani njira, cotsani cokhumudwitsa m'njira mwa anthu anga.