Isaiah 57:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu oipa ali ngati nyanja yoŵinduka, yosatha kukhala bata, ndipo mafunde ake amangoponya matope ndi ndere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma oipa ali ofanana ndi nyanja yowinduka; pakuti siingapume, ndi madzi ake autsa matope ndi uve.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu oyipa ali ngati nyanja yowinduka, yosatha kukhala bata, mafunde ake amaponya matope ndi ndere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma oipa ali ofanana ndi nyanja yowinduka; pakuti siingapume, ndi madzi ace autsa matope ndi ubve.