Isaiah 57:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Senderani kuno, inu anthu ochita zoipa, pakuti muli ngati zidzukulu zam'chigololo, zochokera m'zadama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sendererani kuno chifupi, inu ana amuna a watsenga, mbeu yachigololo ndi yadama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Bwerani kuno, anthu ochita zoyipa, inu muli ngati zidzukulu za mkazi wachigololo ndi wadama!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sendererani kuno cifupi, inu ana amuna a watsenga, mbeu yacigololo ndi yadama.