Isaiah 57:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa phiri lalitali ndi looneka kutali mudakaika bedi kukachita zadama, komwekonso mudakapereka nsembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamwamba pa phiri lalitalitali unayala mphasa yako; kumenekonso wakwera kukapereka nsembe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munayiwala bedi lanu pa phiri lalitali ndi looneka kutali. Mumapita kumeneko kukapereka nsembe zanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamwamba pa phiri lalitaritari unayala mphasa yako; kumenekonso wakwera kukapereka nsembe.