Isaiah 59:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ziwembu zao nzoopsa ngati mazira a mphiri, komanso nzosalimba konse ngati ukonde wa kangaude. Wodya mazira a mphiri amafa. Likasweka dzira limodzi mumatuluka mphiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo afungatira mazira a mphiri aswetse, naluka ukonde wa kangaude; iye amene adya mazira ake amafa, ndi choswanyikacho chisweka nichikhala songo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amayikira mazira a mamba ndipo amaluka ukonde wakangawude. Aliyense amene adzadya mazira awo adzafa, ndipo ngati dzira limodzi lasweka limatulutsa mphiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo afungatira mazira a mamba aswetse, naluka ukonde wa tandaude; iye amene adya mazira ace amafa, ndi coswanyikaco cisweka nicikhala songo.