Isaiah 6:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamenepo ndidafunsa kuti, “Zimenezo ndi mpaka liti, Inu Ambuye?” Iwo adati: “Mpaka mizinda itasanduka mabwinja, mpaka nyumba zitasoŵa anthu okhalamo, mpaka dziko litasanduka chipululu ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pompo ndinati ine, Ambuye mpaka liti? Ndipo anayankha, Mpaka midzi ikhala bwinja, yopanda wokhalamo, ndi nyumba zopanda munthu, ndi dziko likhala bwinja ndithu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo ine ndinati, “Zimenezo ndi mpaka liti Inu Ambuye?” Ndipo Iyeyo anandiyankha kuti, “Mpaka mizinda itasanduka mabwinja nʼkusowa wokhalamo, mpaka nyumba zitasowa anthu okhalamo, mpaka dziko litasanduka chipululu ndithu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pompo ndinati ine, Ambuye mpaka liti? Ndipo anayankha, Mpaka midzi ikhala bwinja, yopanda wokhalamo, ndi nyumba zopanda munthu, ndi dziko likhala bwinja ndithu,