Isaiah 6:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine anthuŵa ndidzaŵasamutsira kutali, ndipo dziko lidzakhala thengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo Yehova wasunthira anthu kutali, ndi mabwinja adzachuluka pakati pa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mpaka Yehova atasamutsira aliyense kutali, dziko nʼkusiyidwa kwathunthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo Yehova wasunthira anthu kutari, ndi mabwinja adzacuruka pakati pa dziko.