Isaiah 6:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ngakhale chigawo chachikhumi cha anthu chitsaleko m'dzikomo, nachonso chidzayatsidwa moto. Koma monga mitengo ya muŵanga ndi ya thundu imasiya chitsa akaidula, chonchonso mbeu yoyera ija idzatsalira ngati chitsa chotsala m'dziko.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo likatsala limodzi la magawo khumi m'menemo, lidzadyedwanso; monga kachere, ndi monganso thundu, imene tsinde lake likhalabe ataigwetsa; chotero mbeu yopatulika ndiyo tsinde lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ngakhale chigawo chakhumi cha anthu chitatsala mʼdziko, nachonso chidzawonongedwa. Koma monga momwe mitengo ya muwanga ndi thundu imasiyira chitsa pamene ayidula, chonchonso mbewu yoyera idzatsalira ngati chitsa chotsala mʼdziko.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo likatsala limodzi la magawo khumi m'menemo, lidzadyedwanso; monga kacere, ndi monganso thundu, imene tsinde lace likhalabe ataigwetsa; cotero mbeu yopatulika ndiyo tsinde lace.