Isaiah 6:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha kufuulako maziko a zitseko ndi ziwundo adagwedezeka ndipo m'Nyumba ya Chautamo mudangoti utsi pha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo maziko a ziundo anasunthika ndi mau amene anafuula, ndipo nyumba inadzazidwa ndi utsi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha kufuwulako maziko a zitseko ndi ziwundo anagwedezeka ndipo mʼNyumba ya Yehova munadzaza utsi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo maziko a ziundo anasunthika ndi mau amene anapfuula, ndipo nyumba inadzazidwa ndi utsi.