Isaiah 6:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Ambuyewo adati, “Pita, kaŵauze anthu ameneŵa kuti, ‘Kumva muzimva, koma osamvetsa. Kupenya muzipenya, koma osazindikira.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anati, Kauze anthu awa, Imvani inu ndithu, koma osazindikira; yang'anani inu ndithu, koma osadziwitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anati, “Pita ndipo ukawawuze anthu awa: “ ‘Kumva muzimva, koma osamvetsetsa; kupenya muzipenya koma osaona kanthu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anati, Kauze anthu awa, Imvani inu ndithu, koma osazindikira; yang'anani inu ndithu, koma osadziwitsa.