Isaiah 60:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi nzinthu zanji zikuti yakaliyakali ngati mitambozi, zikuchita ngati nkhunda zobwerera kumakomo kwakezi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani awa amene auluka ngati mtambo, ndi monga nkhunda kumazenera ao?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi ndi zayani izo zikuwuluka ngati mitambo, ngati kapena nkhunda zobwerera ku zisa zawo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani awa amene auluka ngati mtambo, ndi monga nkhunda ku mazenera ao?