Isaiah 61:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu achilendo adzakutumikirani, ndipo adzaŵeta ziŵeto zanu, iwo omwewo adzalima minda yanu, makamaka minda yanu yamphesa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo alendo adzaimirira ndi kudyetsa magulu ako, ndi anthu akunja adzakhala olima ako, ndi kukukonzera minda yamphesa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu achilendo adzakutumikirani; adzazidyetsa ziweto zanu; iwo adzagwira ntchito mʼminda yanu ya mpesa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo alendo adzaimirira ndi kudyetsa magulu ako, ndi anthu akunja adzakhala olima ako, ndi kukukonzera minda yamphesa.