Isaiah 62:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzakhala ngati chisoti chaufumu chokongola m'manja mwa Chauta, ngati nsangamutu yaulemerero m'manja mwa Mulungu wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe udzakhalanso korona wokongola m'dzanja la Yehova, korona wachifumu m'dzanja la Mulungu wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Udzakhala ngati chipewa chaulemerero mʼdzanja la Yehova, ndi ngati nduwira yaufumu mʼdzanja la Mulungu wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe udzakhalanso korona wokongola m'dzanja la Yehova, korona wacifumu m'dzanja la Mulungu wako.