Isaiah 62:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe Yerusalemu, pa malinga ako ndaikapo alonda, usana wonse ndi usiku wonse sadzakhala chete. Inu amene mumakumbutsa Chauta za malonjezo ake, musapumule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndaika alonda pa malinga ako, Yerusalemu; iwo sadzakhala chete usana pena usiku; inu akukumbutsa Yehova musakhale chete,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe Yerusalemu, pa malinga ako ndayikapo alonda; sadzakhala chete usana kapena usiku. Inu amene mumakumbutsa Yehova za malonjezo ake musapumule.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndaika alonda pa malinga ako, Yerusalemu; iwo sadzakhala cete usana pena usiku; inu akukumbutsa Yehova musakhale cete,