Isaiah 63:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵayendetsa pa nyanja pouma, ndipo monga kavalo woyenda m'chipululu, iwo sadakhumudwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene anawatsogolera kupitira mwa kuya monga kavalo m'chipululu osaphunthwa iwo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene anawayendetsa pa nyanja yozama? Monga kavalo woyendayenda mʼchipululu, iwo sanapunthwe;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene anawatsogolera kupitira mwa kuya monga kavalo m'cipululu osapunthwa iwo?