Isaiah 63:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta kumwambako, ku malo anu oyera ndi aulemerero, mutiyang'ane ife. Kodi chisamaliro chanu chili kuti? Mphamvu zanu zili kuti? Simukutiwonetsanso chikondi chanu ndi chifundo chanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tayang'anani kunsi, taonani pokhala panu poyera, ndi pa ulemerero wanu, changu chanu ndi ntchito zanu zamphamvu zili kuti? Mwanditsekerezera zofunafuna za mtima wanu ndi chisoni chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu Yehova amene muli kumwambako, pa mpando wanu wolemekezeka, wopatulika ndi waulemerero, tiyangʼaneni ife. Kodi changu chanu ndi mphamvu zanu zili kuti? Simukutionetsanso kukoma mtima kwanu ndi chifundo chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tayang'anani kunsi, taonani pokhala panu poyera, ndi pa ulemerero wanu, cangu canu ndi nchito zanu zamphamvu ziri kuti? mwanditsekerezera zofunafuna za mtima wanu ndi cisoni canu.