Isaiah 63:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mukutisokeretsa pa njira zanu? Bwanji mukutilola kuti tizikhala ouma mtima kotero kuti sitikukuwopaninso? Bwererani chifukwa cha atumiki anu, mafuko a anthu amene ali choloŵa chanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova bwanji mwatisocheretsa kusiya njira zanu, ndi kuumitsa mitima yathu tisakuopeni? Bwerani, chifukwa cha atumiki anu, mafuko a cholowa chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani, Inu Yehova, mukutisocheretsa pa njira zanu? Bwanji mukutilola kuti tikhale owuma mitima kotero kuti sitikukuopaninso? Bwererani chifukwa cha atumiki anu; mafuko a anthu amene ali cholowa chanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova bwanji mwatisoceretsa kusiya njira zanu, ndi kuumitsa mitima yathu tisakuopeni? Bwerani, cifukwa ca atumiki anu, mafuko a colowa canu.