Isaiah 63:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tasanduka ngati anthu amene simudatilamulepo, ngati kuti sitidakhalepo anthu anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ife takhala ngati iwo amene simunawalamulira konse, ngati iwo amene sanatchedwe dzina lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tili ngati anthu amene simunawalamulirepo ngati iwo amene sanakhalepo anthu anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ife takhala ngati iwo amene simunawalamulira konse, ngati iwo amene sanachedwa dzina lanu.