Isaiah 63:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumtima mwanga ndidatsimikiza kuti lafika tsiku loti ndilange adani anga molipsira, chafika chaka choti ndipulumutse anthu anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti tsiku lakubwezera lili mumtima mwanga, ndi chaka cha kuombola anthu anga chafika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndinatsimikiza mu mtima mwanga kuti lafika tsiku lolipsira anthu anga; ndipo chaka cha kuwomboledwa kwanga chafika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti tsiku lakubwezera liri mumtima mwanga, ndi caka ca kuombola anthu anga cafika.