Isaiah 63:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidapondereza anthu a mitundu ina ndili wokwiya, ndipo ndidaŵasakaza. Magazi ao ndidaŵathira pansi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinapondereza anthu m'kukwiya kwanga, ndi kuwatswanya mu ukali wanga, ndi kutsanulira mwazi wa moyo wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinapondereza mitundu ya anthu ndili wokwiya; ndipo ndinawasakaza ndipo ndinathira magazi awo pansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinapondereza anthu m'kukwiya kwanga, ndi kuwatswanya mu ukali wanga, ndi kutsanulira mwazi wa moyo wao.