Isaiah 64:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
monga momwe moto umatenthera tchire, ndiponso monga momwe umagadutsira madzi, kuti adani anu akudziŵeni, ndipo kuti anthu a mitundu ina anjenjemere pamaso panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga pamene moto uyatsa zitsamba, ndi moto uwiritsa madzi; kudziwitsa kwa amaliwongo anu dzina lanu, kuti amitundu anthunthumire pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe moto umatenthera tchire ndiponso kuwiritsa madzi, tsikani kuti adani anu adziwe dzina lanu, ndiponso kuti mitundu ya anthu injenjemere pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga pamene moto uyatsa zitsamba, ndi moto uwiritsa madzi; kudziwitsa kwa amaliwongo anu dzina lanu, kuti amitundu anthunthumire pamaso panu,