Isaiah 64:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi ina yake mudatsika pansi pano kudzachita zinthu zoopsa zimene sitidaziyembekeze. Mapiri atakuwonani, adanjenjemera ndi mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Inu munachita zinthu zoopsa, zimene ife sitinayang'anira, Inu munatsika, mapiri anagwedezeka pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti nthawi ina pamene munatsika munachita zinthu zoopsa zimene sitinaziyembekezere, ndipo mapiri anagwedezeka pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Inu munacita zinthu zoopsya, zimene ife sitinayang'anira, Inu munatsika, mapiri anagwedezeka pamaso panu.