Isaiah 64:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe amene amatamira dzina lanu popemphera, kapena amene amatekeseka nzopempha chithandizo kwa Inu. Mwatifulatira ndipo mwatisandutsa akapolo a machimo athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo palibe amene aitana dzina lanu, amene adzikakamiza yekha kugwiritsa Inu; pakuti Inu mwatibisira nkhope yanu, ndipo mwatinyeketsa ndi zoipa zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe amene amapemphera kwa Inu kutekeseka kuti apemphe chithandizo kwa Inu; pakuti mwatifulatira ndi kutisiya chifukwa cha machimo athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo palibe amene aitana dzina lanu, amene adzikangamiza yekha kugwiritsa Inu; pakuti Inu mwatibisira nkhope yanu, ndipo mwatinyeketsa ndi zoipa zathu.